|
| 1 |
|
| Adamu adabereka Seti, Seti adabereka Enosi, Enosi adabereka Kenani, |
|
| 2 |
|
| Kenani adabereka Mahalalele, Mahalalele adabereka Yaredi, |
|
| 3 |
|
| Yaredi adabereka Enoki, Enoki adabereka Metusela, Metusela adabereka Lameki, |
|
| 4 |
|
| Lameki adabereka Nowa, Nowa adabereka Semu, Hamu ndi Yafeti. |
|
| 5 |
|
| Ana a Yafeti naŵa: Gomeri, Magogi, Madai, Yavani, Tubala, Meseki ndi Tirasi. |
|
| 6 |
|
| Ana a Gomeri naŵa: Asikenazi, Rifati ndi Togarima. |
|
| 7 |
|
| Ana a Yavani naŵa: Elisa, Tarisisi, Kitimu ndi Rodanimu. |
|
| 8 |
|
| Ana a Hamu naŵa: Kusi, Ejipito, Puti ndi Kanani. |
|
| 9 |
|
| Ana a Kusi naŵa: Seba, Havila, Sabita, Raama ndi Sabiteka. Ana a Raama naŵa: Sheba ndi Dedani. |
|
| 10 |
|
| Kusi adabereka Nimirodi. Iyeyu ndiye adayamba kukhala munthu wamphamvu pa dziko lonse lapansi. |
|
| 11 |
|
| Ejipito adabereka Ludimu, Anamimu, Lehabimu, Nafituhimu, |
|
| 12 |
|
| Patirusimu, Kasiluhimu (kholo la Afilisti) ndi Kafitorimu. |
|
| 13 |
|
| Kanani adabereka Sidoni mwana wake wachisamba ndi Heti. |
|
| 14 |
|
| Kanani analinso kholo la Ayebusi, Aamori, Agirigasi, |
|
| 15 |
|
| Ahivi, Aariki, Asini, |
|
| 16 |
|
| Arivadi, Azemari ndi Ahamati. |
|
| 17 |
|
| Ana a Semu naŵa: Elamu, Asuri, Aripakisadi, Ludi, Aramu, Uzi, Huli, Getere ndi Meseki. |
|
| 18 |
|
| Aripakisadi adabereka Sela. Sela adabereka Ebere. |
|
| 19 |
|
| Ebere adabereka ana aamuna aŵiri. Mwana wina anali Pelegi (pakuti anthu adaagaŵikana pa nthaŵi yake), ndipo mbale wake anali Yokotani. |
|
| 20 |
|
| Yokotani adabereka Alimodadi, Selefi, Hazara-Maveti, Yera, |
|
| 21 |
|
| Hadoramu, Uzali, Dikila, |
|
| 22 |
|
| Ebala, Abimaele, Sheba, |
|
| 23 |
|
| Ofiri, Havila ndi Yobabu. Onseŵa anali ana a Yokotani. |
|
| 24 |
|
| A m'banja la Semu anali aŵa: Aripakisadi, Sela, |
|
| 25 |
|
| Ebere, Pelegi, Reu, |
|
| 26 |
|
| Serugi, Nahori, Tera, |
|
| 27 |
|
| ndi Abramu, ndiye kuti Abrahamu. |
|
| 28 |
|
| Ana a Abrahamu naŵa: Isaki ndi Ismaele. |
|
| 29 |
|
| Mibadwo yao nayi: mwana wachisamba wa Ismaele anali Nebayoti. Panalinso Kedara, Adibeele, Mibisamu, |
|
| 30 |
|
| Misima, Duma, Masa, Hadadi, Tema, |
|
| 31 |
|
| Yeturi, Nafisi ndi Kedema. |
|
| 32 |
|
| Ana a Ketura mzikazi wa Abrahamu naŵa: Zimirani, Yokosamu, Medani, Midiyani, Isibaki, ndiponso Suwa. Ana a Yokosamu naŵa: Sheba ndi Dedani. |
|
| 33 |
|
| Ana a Midiyani naŵa: Efa, Efere, Hanoki, Abida ndi Elida. Onseŵa anali zidzukulu za Ketura. |
|
| 34 |
|
| Abrahamu adabereka Isaki. Ana a Isaki naŵa: Esau ndi Israele. |
|
| 35 |
|
| Ana a Esau naŵa: Elifazi, Reuele, Yeusi, Yalamu ndi Kora. |
|
| 36 |
|
| Ana a Elifazi naŵa: Temani, Omara, Zefi, Gatamu, Kenazi, Timna ndi Amaleke. |
|
| 37 |
|
| Ana a Reuele naŵa: Nahati, Zera, Sama ndi Miza. |
|
| 38 |
|
| Ana a Seiri naŵa: Lotani, Sobala, Zibiyoni, Ana, Disoni, Ezere ndi Disani. |
|
| 39 |
|
| Ana a Lotani naŵa: Hori ndi Honamu. Mlongo wake wa Lotani anali Timna. |
|
| 40 |
|
| Ana a Sobala naŵa: Aliyani, Manahati, Ebala, Sefi ndi Onamu. Ana a Zibiyoni naŵa: Aiya ndi Ana. |
|
| 41 |
|
| Mwana wa Ana anali Disoni. Ana a Disoni naŵa: Hamurani, Esibani, Itirani, ndi Kerani. |
|
| 42 |
|
| Ana a Ezere naŵa: Bilihani, Zaavani ndi Yaakani. Ana a Disani naŵa: Uzi ndi Arani. |
|
| 43 |
|
| Naŵa mafumu amene ankalamulira ku dziko la Edomu, Aisraele adakalibe mfumu iliyonse: Bela mwana wa Beori, ndipo mzinda wake unali Dinaba. |
|
| 44 |
|
| Bela atafa, Yobabu mwana wa Zera wa ku Bozira, adaloŵa ufumu m'malo mwake. |
|
| 45 |
|
| Yobabu atafa, Husamu wa ku dziko la Temani adaloŵa ufumu m'malo mwake. |
|
| 46 |
|
| Husamu atafa, Hadadi mwana wa Bedadi, amene adagonjetsa Amidiyani ku dziko la Mowabu, adaloŵa ufumu m'malo mwake. Mzinda wake ankautchula kuti Aviti. |
|
| 47 |
|
| Hadadi atafa, Samila wa ku Masireka adaloŵa ufumu m'malo mwake. |
|
| 48 |
|
| Samila atafa, Shaulo wa ku Rehoboti ku Yufurate, adaloŵa ufumu m'malo mwake. |
|
| 49 |
|
| Shaulo atafa, Baala-Hanani mwana wa Akibori adaloŵa ufumu m'malo mwake. |
|
| 50 |
|
| Baala-Hanani atafa, Hadadi adaloŵa ufumu m'malo mwake. Mzinda wake ankautchula kuti Pai. Mkazi wake anali Metabele mwana wa Materedi, mwana wa Mezahabu. |
|
| 51 |
|
| Hadadi nayenso nkufa. Mafumu a ku Edomu anali aŵa: Timna, Aliva, Yeteti, |
|
| 52 |
|
| Oholibama, Ela, Pinoni, |
|
| 53 |
|
| Kenazi, Temani, Mibizara, |
|
| 54 |
|
| Magadiele ndi Iramu. Ameneŵa ndiwo mafumu a ku Edomu. |
|
|
|
|