|
| 1 |
|
| Benjamini adabereka Bela mwana wake wachisamba, Asibele mwana wake wachiŵiri, Ahara mwana wake wachitatu, |
|
| 2 |
|
| Noha mwana wake wachinai ndi Rafa mwana wake wachisanu. |
|
| 3 |
|
| Bela anali ndi zidzukulu izi: Adara, Gera, Abihudi, |
|
| 4 |
|
| Abisuwa, Namani, Ahowa, |
|
| 5 |
|
| Gera, Sefufani ndiponso Huramu. |
|
| 6 |
|
| Ana a Ehudi amene anali atsogoleri a mabanja okhala ku Geba, adachotsedwa kwaoko ndipo adakakhala ku Manahati. |
|
| 7 |
|
| Anawo anali Namani, Ahiya ndi Gera. Gerayo amene anali bambo wake wa Uza ndi Ahihudi, ndiye adatsogolera anthu osamutsidwawo. |
|
| 8 |
|
| Saharaimu, atachotsa akazi ake Husimu ndi Baara, adakhala ndi ana m'dziko la Mowabu. |
|
| 9 |
|
| Mwa mkazi wake Hodesi adabelekamo ana aŵa: Yobabu, Zibiya, Mesa, Malikamu, |
|
| 10 |
|
| Yeuzi, Sakiya ndi Mirima. Ameneŵa ndiwo amene anali ana ake, atsogoleri a mabanja. |
|
| 11 |
|
| Mwa Husimu adaberekamonso ana aŵa: Abitubu, ndi Elipaala. |
|
| 12 |
|
| Ana a Elipaala naŵa: Ebere, Misamu ndi Semedi. Semedi ndiye adamanga mizinda ya Ono ndi Lodi pamodzi ndi midzi yake yomwe. |
|
| 13 |
|
| Beriya ndi Sema anali atsogoleri a mabanja okhala ku mzinda wa Aiyaloni. Iwowo adathaŵitsa nzika za ku Gati. |
|
| 14 |
|
| Zidzukulu zina za Beriya zinali Ahiyo, Sasaki, Yeremoti, |
|
| 15 |
|
| Zebadiya, Aradi, Edere, |
|
| 16 |
|
| Mikaele, Isipa ndi Yoha. |
|
| 17 |
|
| Zebadiya, Mesulamu, Hiziki, Hebere, |
|
| 18 |
|
| Isimerai, Iziliya ndi Yobabu anali zidzukulu za Elipaala. |
|
| 19 |
|
| Yakimu, Zikiri, Zabidi, |
|
| 20 |
|
| Eliyenai, Ziletai, Eliyele, |
|
| 21 |
|
| Adaya, Beraya ndi Simiratu anali zidzukulu za Simei. |
|
| 22 |
|
| Isipani, Ebere, Eliyele, |
|
| 23 |
|
| Abidoni, Zikiri, Hanani, |
|
| 24 |
|
| Hananiya, Elamu, Anitotiya, |
|
| 25 |
|
| Ifidea ndi Penuwele, anali zidzukulu za Sasaki. |
|
| 26 |
|
| Samuserai, Sehariya, Ataliya, |
|
| 27 |
|
| Yaaresiya, Eliya ndi Zikiri anali zidzukulu za Yerohamu. |
|
| 28 |
|
| Ameneŵa ndiwo amene anali atsogoleri a mabanja, anthu otchuka potsata mibadwo yao, ndipo onsewo ankakhala ku Yerusalemu. |
|
| 29 |
|
| Yeiyele, amene adaamanga Gibiyoni, ankakhala ku Gibiyoni komweko. Mkazi wake anali Maaka. |
|
| 30 |
|
| Mwana wake wachisamba anali Abidoni, pambuyo pa iyeyo panali Zuri, Kisi, Baala, Nere, Nadabu, |
|
| 31 |
|
| Gedori, Ahiyo, Zekeri, |
|
| 32 |
|
| ndi Mikiloti bambo wa Simea). Tsono, monga achibale ao aja, iwoŵanso ankakhala ku Yerusalemu pamodzi ndi achibale aowo. |
|
| 33 |
|
| Nere adabereka Kisi, Kisi adabereka Mfumu Saulo, Mfumu Saulo adabereka Yonatani, Malikisuwa, Abinadabu, ndi Esibaala. |
|
| 34 |
|
| Yonatani adabereka Meribaala. Meribaala adabereka Mika. |
|
| 35 |
|
| Ana a Mika naŵa: Pitoni, Meleki, Tareya ndi Ahazi. |
|
| 36 |
|
| Ahazi adabereka Yehoyada, Yehoyada adabereka Alemeti, Azimaveti ndi Zimiri. Zimiri adabereka Moza, |
|
| 37 |
|
| Moza adabereka Bineya, Bineya adabereka Rafa, Rafa adabereka Eleasa, Eleasa adabereka Azele. |
|
| 38 |
|
| Azele anali ndi ana asanu ndi mmodzi, ndipo maina ao naŵa: Azirikamu, Bokeru, Ismaele, Seyariya, Obadiya ndi Hanani. Onseŵa anali ana a Azele. |
|
| 39 |
|
| Ana a mbale wake Eseki naŵa: mwana wake wachisamba Ulamu, wachiŵiri Yeusi, wachitatu Elifeleti. |
|
| 40 |
|
| Ana a Ulamu anali ankhondo amphamvu, anthu amauta, ndipo anali ndi ana ndi adzikulu 150. Onseŵa anali Abenjamini. |
|
|
|
|