Buku Lopatulika 1992
|
| 1 |
| Pfuulirani kwa Yehova, inu, dziko lonse lapansi. |
| 2 |
| Tumikirani Yehova ndi cikondwerero: Idzani pamaso pace ndi kumyimbira mokondwera, |
| 3 |
| Dziwani kuti Yehova ndiye Mulungu; Iyeyu anatilenga, ndipo ife ndife ace; Ndife anthu ace ndi nkhosa za pabusa pace. |
| 4 |
| Lowani ku zipata zace ndi ciyamiko, Ndi ku mabwalo ace ndi cilemekezo: Myamikeni; lilemekezeni dzina lace. |
| 5 |
| Pakuti Yehova ndiye wabwino; cifundo cace cimamka muyaya; Ndi cikhulupiriko cace ku mibadwo mibadwo. |
| Sungani Zolemba |
https://beblia.bible:81/BibleAudio/chewa1992/psalms/100.mp3
150
100