× Chilankhulo Europe Chirasha Chibelarusi Chiyukireniya Chipolishi Chiserbia Chibugariya Chislovakia Czech Chiromani Chi Moldova Azerbaijan Chiameniya Chijojiya Chialubaniya Avar Bashkir Chitata Chechen Chisiloveniya Chiroatia ChiEstonia Chilativiya Chilithuania Chihangare Chifinishi Chinorway Chiswedwe Chi Icelandic Chi Greek Chimakedoniya Chijeremani Bavarian Chidatchi Chidanishi Chiwelsh Chi Gaelic Chiairishi Chifalansa Basque Chikatalani Chitaliyana Chitchainizi Achiroma Bosnian Kabardian Kumpoto kwa Amerika Chingerezi South America Chisipanishi Chipwitikizi Chiguarani Quechuan Aymara Central America Chaku Jamaican Chilankhulo Chichewa Qeqchi Chaku Haiti Kum'mawa kwa Asia Chitchaina Chijapani Korea Chimongoliya Uyghur Hmong Tibetian South East Asia Chimalaysian Chibama Chin Chinepali Cebuano Chitagalogi Wachikambodiya Chi Thai Chiindoneziya Chisunda Chivietinamu Chijava Lao Iban IuMien Kachin Lahu Aceh Balinese Bugis Pampanga Sasak Shan Waray Madurese Kumwera kwa Asia Chihindi Оdia Awadhi Mizo Chikannada Malayalam Kambikatha Chimarathi Chigujarati Tamil Chilankhulo Chipunjabi Kurukh Assamese Maithili Chibengali Chiurdu Sinhala Dogri Haryanvi Meitei Konkani Santali Sindhi Koya Thado Sanskrit Devanagari Adilabad Gondi Ahirani Balochi Bundeli Chhattisgarhi Garhwali Kangri Kumaoni Mewari Munda Sadri Seraiki Shekhawati Sylheti Bagri Bhilali Bodo Braj Tulu Central Asia Chikigizi Chiuzbeki Chitajik Anthu aku Turkmen Kazakhstan Karakalpak Kuulaya Chituruki Chihebri Chiarabu Persian Chikurdi Mazanderani Chiashto Chikoputiki Africa Chiafrikaana Chixhosa Chizulu Ndebele Sotho Chiamhariki Wolaytta Waku Nigeria Mossi Ika Dinka Kabyle Ewe Chiswahili Morocco Wachisomali Chishona Madagascar Chiigbo Lingala Baoule Chiswati Chitsonga Chitswana Gambia Chiyoruba Kamba Chikinyarwanda Chihausa Chewa Chiluo Makua Dyula Fulfulde Kalenjin Kikuyu Kikwango Kirundi Krio Nigerian Pidgin Oromo Tshiluba Tshivenda Twi Umbundu Lugbara Luguru Pular Gussi Maasai Turkana Moba Nuer Shilluk Tamasheq Makonde Bemba Fon Hadiyya Ibibio Kimbundu Kimiiru Lango Liberian Kreyol Lomwe Mende Morisyen Ndau Nyankole Sena Sidamo Soga Songe Sukuma Tarifit Teso Tiv Zande Dagbani Edo Kituba Dziko la Australia New Zealand Papua New Guinea Ziyankhulo Zakale Chiaramu Chilatini Chiesperanto 1 1 1 BL 1992 2016Buku Lopatulika 2014BL 1992BLYDC1 1 1 MASALIMO GENESISEKSODOLEVITIKONUMERIDEUTERONOMOYOSWAOWERUZARUTE1 SAMUELE2 SAMUELE1 MAFUMU2 MAFUMU1 MBIRI2 MBIRIEZARANEHEMIYAESTEREYOBUMASALIMOMIYAMBOMLALIKINYIMBO YA SOLOMONIYESAYAYEREMIYAMALIROEZEKIELEDANIELEHOSEYAYOWELEAMOSIOBADIYAYONAMIKANAHUMUHABAKUKUZEFANIYAHAGAIZEKARIYAMALAKI--- --- ---MATEYUMARKOLUKAYOHANEMACHITIDWE A ATUMWIAROMA1 AKORINTO2 AKORINTOAGALATIYAAEFESOAFILIPIAKOLOSE1 ATESALONIKA2 ATESALONIKA1 TIMOTEO2 TIMOTEOTITOFILEMONIAHEBRIYAKOBO1 PETRO2 PETRO1 YOHANE2 YOHANE3 YOHANEYUDACHIVUMBULUTSO1 1 1 107 1234567891011121314151617181920212223242526272829303132333435363738394041424344454647484950515253545556575859606162636465666768697071727374757677787980818283848586878889909192939495969798991001011021031041051061071081091101111121131141151161171181191201211221231241251261271281291301311321331341351361371381391401411421431441451461471481491501 1 1 : 33 123456789101112131415161718192021222324252627282930313233343536373839404142431 1 1 Buku Lopatulika MASALIMO 107 Sungani Zolemba 1Yamikani Yehova pakuti Iye ndiye wabwino; Pakuti cifundo cace ncosatha.2Atere oomboledwa a Yehova, Amene anawaombola m'dzanja la wosautsa;3Nawasokolotsa kumaiko, Kucokera kum'mawa ndi kumadzulo, Kumpoto ndi kunyanja.4Anasokera m'cipululu, m'njira yopanda anthu; Osapeza mudzi wokhalamo.5Anamva njala ndi ludzu, Moyo wao unakomoka m'kati mwao.6Pamenepo anapfuulira kwa Yehova mumsauko mwao, Ndipo anawalanditsa m'kupsinjika kwao.7Ndipo anawatsogolera pa njira yolunjika, Kuti amuke ku mudzi wokhalamo.8Ayamike Yehova cifukwa ca cifundo cace, Ndi zodabwiza zace za kwa ana a anthu!9Pakuti akhutitsa mtima wolakalaka, Nadzaza mtima wanjala ndi zabwino.10Iwo akukhala mumdima ndi mu mthunzi wa imfa, Omangika ndi kuzunzika ndi citsulo;11Popeza anapikisana nao mau a Mulungu, Napeputsa uphungu wa Wam'mwambamwamba;12Kotero kuti anagonjetsa mtima wao ndi cobvuta; Iwowa anakhumudwa koma panalibe mthandizi.13Pamenepo anapfuulira kwa Yehova mumsauko mwao, Ndipo anawapulumutsa m'kupsinjika kwao.14Anawaturutsa mumdima ndi mu mthunzi wa imfa, Nadula zomangira zao.15Ayamike Yehova cifukwa ca cifundo cace, Ndi zodabwiza zace za kwa ana a anthu!16Popeza adaswa zitseko zamkuwa, Natyola mipiringidzo yacitsulo.17Anthu opusa azunzika cifukwa ca zolakwa zao, Ndi cifukwa ca mphulupulu zao.18Mtima wao unyansidwa naco cakudya ciri conse; Ndipo ayandikira zipata za imfa.19Pamenepo apfuulira kwa Yehova m'kusauka kwao, Ndipo awapulumutsa m'kupsinjika kwao.20Atumiza mau ace nawaciritsa, Nawapulumutsa ku cionongeko cao.21Ayamike Yehova cifukwa ca cifundo cace, Ndi zodabwiza zace za kwa ana a anthu!22Ndipo apereke nsembe zaciyamiko, Nafotokozere nchito zace ndi kupfuula mokondwera.23Iwo akutsikira kunyanja nalowa m'zombo, Akucita nchito zao pa madzi akuru;24Iwowa apenya nchito za Yehova, Ndi zodabwiza zace m'madzi ozama.25Popeza anena, nautsa namondwe, Amene autsa mafunde ace.26Akwera kuthambo, atsikira kozama; Mtima wao usungunuka naco coipaco.27Adzandira napambanitsa miyendo ngati munthu woledzeta, Nathedwa nzeru konse.28Pamenepo apfuulira kwa Yehova m'kusauka kwao, Ndipo awaturutsa m'kupsinjika kwao.29Asanduliza namondwe akhale bata, Kotero kuti mafunde ace atonthole.30Pamenepo akondwera, popeza pagwabata; Ndipo Iye awatsogolera kudooko afumko.31Ayamike Yehova cifukwa ca cifundo cace, Ndi zodabwiza zace za kwa ana a anthu!32Amkwezenso mu msonkhano wa anthu, Namlemekeze pokhala akulu.33Asanduliza mitsinje ikhale cipululu, Ndi akasupe a madzi akhale nthaka youma;34Dziko lazipatso, likhale lakhulo, Cifukwa ca coipa ca iwo okhalamo.35Asanduliza cipululu cikhale tha wale, Ndi dziko louma likhale akasupe a madzi.36Ndi apo akhalitsa anjala, Kuti amangeko mudzi wokhalamo anthu;37Nafese m'minda, naoke mipesa, Ndiyo vakubata zipatso zolemeza.38Ndipo awadalitsa, kotero kuti, acuruka kwambiri; Osacepsanso zoweta zao.39Koma acepanso, nawerama, Cifukwa ca cisautso, coipa ndi cisoni.40Atsanulira cimpepulo pa akulu, Nawasokeretsa m'cipululu mopanda njira.41Koma aika waumphawi pamsanje posazunzika, Nampatsa mabanja ngati gulu la nkhosa.42Oongoka mtima adzaciona nadzasekera; Koma cosalungama conse citseka pakamwa pace.43Wokhala nazo nzeru asamalire izi, Ndipo azindikire zacifundo za Yehova,Chewa Bible (BL) 1992 Zambia Bible Society, Malawi Bible Society and Zimbabwe Bible Society Buku Lopatulika MASALIMO 107 00:00:00 00:00:00 0.5x 2.0x https://beblia.bible:81/BibleAudio/chewa1992/psalms/107.mp3 150 107