× Chilankhulo Europe Chirasha Chibelarusi Chiyukireniya Chipolishi Chiserbia Chibugariya Chislovakia Czech Chiromani Chi Moldova Azerbaijan Chiameniya Chijojiya Chialubaniya Avar Bashkir Chitata Chechen Chisiloveniya Chiroatia ChiEstonia Chilativiya Chilithuania Chihangare Chifinishi Chinorway Chiswedwe Chi Icelandic Chi Greek Chimakedoniya Chijeremani Bavarian Chidatchi Chidanishi Chiwelsh Chi Gaelic Chiairishi Chifalansa Basque Chikatalani Chitaliyana Chitchainizi Achiroma Bosnian Kumpoto kwa Amerika Chingerezi South America Chisipanishi Chipwitikizi Chiguarani Quechuan Aymara Central America Chaku Jamaican Chilankhulo Chichewa Qeqchi Chaku Haiti Kum'mawa kwa Asia Chitchaina Chijapani Korea Chimongoliya Uyghur Hmong South East Asia Chimalaysian Chibama Chin Chinepali Cebuano Chitagalogi Wachikambodiya Chi Thai Chiindoneziya Chivietinamu Chijava Lao Iban IuMien Kachin Lahu Aceh Balinese Bugis Pampanga Sasak Shan Waray Kumwera kwa Asia Chihindi Оdia Awadhi Mizo Chikannada Malayalam Kambikatha Chimarathi Chigujarati Tamil Chilankhulo Chipunjabi Kurukh Assamese Maithili Chibengali Chiurdu Sinhala Dogri Haryanvi Meitei Konkani Santali Sindhi Koya Thado Sanskrit Devanagari Adilabad Gondi Ahirani Balochi Bundeli Chhattisgarhi Garhwali Kangri Kumaoni Mewari Munda Sadri Seraiki Shekhawati Sylheti Central Asia Chikigizi Chiuzbeki Chitajik Anthu aku Turkmen Kazakhstan Karakalpak Kuulaya Chituruki Chihebri Chiarabu Persian Chikurdi Chiashto Chikoputiki Africa Chiafrikaana Chixhosa Chizulu Ndebele Sotho Chiamhariki Wolaytta Waku Nigeria Mossi Ika Dinka Kabyle Ewe Chiswahili Morocco Wachisomali Chishona Madagascar Chiigbo Lingala Baoule Chiswati Chitsonga Chitswana Gambia Chiyoruba Kamba Chikinyarwanda Chihausa Chewa Chiluo Makua Dyula Fulfulde Kalenjin Kikuyu Kikwango Kirundi Krio Nigerian Pidgin Oromo Tshiluba Tshivenda Twi Umbundu Lugbara Luguru Pular Gussi Maasai Turkana Moba Nuer Shilluk Tamasheq Makonde Bemba Fon Hadiyya Ibibio Kimbundu Kimiiru Lango Liberian Kreyol Lomwe Mende Morisyen Ndau Nyankole Sena Sidamo Soga Songe Sukuma Tarifit Teso Tiv Zande Dziko la Australia New Zealand Papua New Guinea Ziyankhulo Zakale Chiaramu Chilatini Chiesperanto 1 1 1 BL 1992 2016Buku Lopatulika 2014BL 1992BLYDC1 1 1 MIYAMBO GENESISEKSODOLEVITIKONUMERIDEUTERONOMOYOSWAOWERUZARUTE1 SAMUELE2 SAMUELE1 MAFUMU2 MAFUMU1 MBIRI2 MBIRIEZARANEHEMIYAESTEREYOBUMASALIMOMIYAMBOMLALIKINYIMBO YA SOLOMONIYESAYAYEREMIYAMALIROEZEKIELEDANIELEHOSEYAYOWELEAMOSIOBADIYAYONAMIKANAHUMUHABAKUKUZEFANIYAHAGAIZEKARIYAMALAKI--- --- ---MATEYUMARKOLUKAYOHANEMACHITIDWE A ATUMWIAROMA1 AKORINTO2 AKORINTOAGALATIYAAEFESOAFILIPIAKOLOSE1 ATESALONIKA2 ATESALONIKA1 TIMOTEO2 TIMOTEOTITOFILEMONIAHEBRIYAKOBO1 PETRO2 PETRO1 YOHANE2 YOHANE3 YOHANEYUDACHIVUMBULUTSO1 1 1 1 123456789101112131415161718192021222324252627282930311 1 1 : 1 1234567891011121314151617181920212223242526272829303132331 1 1 Buku Lopatulika MIYAMBO 1 Sungani Zolemba 1MIYAMBI ya Solomo mwana wa Davide, mfumu ya Israyeli.2Kudziwa nzeru ndi mwambo; Kuzindikira mau ozindikiritsa;3Kulandira mwambo wakusamalira macitidwe, Cilungamo, ciweruzo ndi zolunjika;4Kucenjeza acibwana, Kuphunzitsa mnyamata kudziwa ndi kulingalira;5Kuti wanzeru amve, naonjezere kuphunzira; Ndi kuti wozindikira afikire kuuphungu;6Kuzindikira mwambi ndi tanthauzo lace, Mau a anzeru, ndi zophiphiritsa zao.7Kuopa Yehova ndiko ciyambi ca kudziwa; Opusa anyoza nzeru ndi mwambo.8Mwananga, tamva mwambo wa atate wako, Ndi kusasiya cilangizo ca amako9Pakuti izi ndi korona wa cisomo pamtu pako, Ndi mkanda pakhosi pako.10Mwananga, akakukopa ocimwa usalole.11Akanena, Idza nafe, tibisalire mwazi, Tilalire osacimwa opanda cifukwa;12Tiwameze ali ndi moyo ngati manda, Ali amphumphu, ngati akutsikira kudzenje;13Tidzapeza cuma conse ca mtengo wace, Tidzadzaza nyumba zathu ndi zofunkha;14Udzacita nafe maere, Tonse tidzakhala ndi cibeti cimodzi;15Mwananga, usayende nao m'njira; Letsa phazi lako ku mayendedwe ao;16Pakuti mapazi ao athamangira zoipa, Afulumira kukhetsa mwazi.17Pakuti kuchera msampha pamaso pa mbalame ndi cabe;18Ndipo awa abisalira mwazi wao wao, alalira miyoyo yao yao.19Mayendedwe a yense wopindula cuma monyenga ngotere; Cilanda moyo wa eni ace,20Nzeru ipfuula panja; Imveketsa mau ace pabwalo;21Iitana posonkhana anthu polowera pacipata; M'mudzi inena mau ace;22Kodi mudzakonda zacibwana kufikira liti, acibwana inu? Onyoza ndi kukonda kunyoza, Opusa ndi kuda nzeru?23Tembenukani pamene ndikudzudzulani; Taonani, nditsanulira pa inu mzimu wanga, Ndikudziwitsani mau anga.24Cifukwa ndaitana, ndipo munakana; Ndatambasula dzanja langa, ndipo panalibe analabadira;25Koma munapeputsa uphungu wangawonse, Ndi kukana kudzudzula kwanga.26Inetu ndidzacitiraciphwete tsoka lanu, Ndidzatonyola pakudza mantha anu;27Pakudza mantha anu ngati mphepo yopasula, Ndi pofika tsoka lanu ngati kabvumvulu; Pakudza kwa inu bvuto ndi nsautso.28Pamenepo adzandiitana, koma sindidzabvomera; Adzandifunatu, osandipeza ai;29Cifukwa anada nzeru, Sanafuna kuopa Yehova;30Anakana uphungu wanga, Nanyoza kudzudzula kwanga konse;31Momwemo adzadya zipatso za mayendedwe ao, Nadzakhuta zolingalira zao.32Pakuti kubwerera m'mbuyo kwa acibwana kudzawapha; Ndipo mphwai za opusa zidzawaononga.33Koma wondimvera ine adzakhala osatekeseka, Nadzakhala phe osaopa zoipa,Chewa Bible (BL) 1992 Zambia Bible Society, Malawi Bible Society and Zimbabwe Bible Society Buku Lopatulika MIYAMBO 1 00:00:00 00:00:00 0.5x 2.0x https://beblia.bible:81/BibleAudio/chewa1992/proverbs/001.mp3 31 1