× Chilankhulo Europe Chirasha Chibelarusi Chiyukireniya Chipolishi Chiserbia Chibugariya Chislovakia Czech Chiromani Chi Moldova Azerbaijan Chiameniya Chijojiya Chialubaniya Avar Bashkir Chitata Chechen Chisiloveniya Chiroatia ChiEstonia Chilativiya Chilithuania Chihangare Chifinishi Chinorway Chiswedwe Chi Icelandic Chi Greek Chimakedoniya Chijeremani Bavarian Chidatchi Chidanishi Chiwelsh Chi Gaelic Chiairishi Chifalansa Basque Chikatalani Chitaliyana Chitchainizi Achiroma Bosnian Kumpoto kwa Amerika Chingerezi South America Chisipanishi Chipwitikizi Chiguarani Quechuan Aymara Central America Chaku Jamaican Chilankhulo Chichewa Qeqchi Chaku Haiti Kum'mawa kwa Asia Chitchaina Chijapani Korea Chimongoliya Uyghur Hmong South East Asia Chimalaysian Chibama Chin Chinepali Cebuano Chitagalogi Wachikambodiya Chi Thai Chiindoneziya Chivietinamu Chijava Lao Iban IuMien Kachin Lahu Aceh Balinese Bugis Pampanga Sasak Shan Waray Kumwera kwa Asia Chihindi Оdia Awadhi Mizo Chikannada Malayalam Kambikatha Chimarathi Chigujarati Tamil Chilankhulo Chipunjabi Kurukh Assamese Maithili Chibengali Chiurdu Sinhala Dogri Haryanvi Meitei Konkani Santali Sindhi Koya Thado Sanskrit Devanagari Adilabad Gondi Ahirani Balochi Bundeli Chhattisgarhi Garhwali Kangri Kumaoni Mewari Munda Sadri Seraiki Shekhawati Sylheti Central Asia Chikigizi Chiuzbeki Chitajik Anthu aku Turkmen Kazakhstan Karakalpak Kuulaya Chituruki Chihebri Chiarabu Persian Chikurdi Chiashto Chikoputiki Africa Chiafrikaana Chixhosa Chizulu Ndebele Sotho Chiamhariki Wolaytta Waku Nigeria Mossi Ika Dinka Kabyle Ewe Chiswahili Morocco Wachisomali Chishona Madagascar Chiigbo Lingala Baoule Chiswati Chitsonga Chitswana Gambia Chiyoruba Kamba Chikinyarwanda Chihausa Chewa Chiluo Makua Dyula Fulfulde Kalenjin Kikuyu Kikwango Kirundi Krio Nigerian Pidgin Oromo Tshiluba Tshivenda Twi Umbundu Lugbara Luguru Pular Gussi Maasai Turkana Moba Nuer Shilluk Tamasheq Makonde Bemba Fon Hadiyya Ibibio Kimbundu Kimiiru Lango Liberian Kreyol Lomwe Mende Morisyen Ndau Nyankole Sena Sidamo Soga Songe Sukuma Tarifit Teso Tiv Zande Dagbani Dziko la Australia New Zealand Papua New Guinea Ziyankhulo Zakale Chiaramu Chilatini Chiesperanto 1 1 1 BL 1992 2016Buku Lopatulika 2014BL 1992BLYDC1 1 1 MIYAMBO GENESISEKSODOLEVITIKONUMERIDEUTERONOMOYOSWAOWERUZARUTE1 SAMUELE2 SAMUELE1 MAFUMU2 MAFUMU1 MBIRI2 MBIRIEZARANEHEMIYAESTEREYOBUMASALIMOMIYAMBOMLALIKINYIMBO YA SOLOMONIYESAYAYEREMIYAMALIROEZEKIELEDANIELEHOSEYAYOWELEAMOSIOBADIYAYONAMIKANAHUMUHABAKUKUZEFANIYAHAGAIZEKARIYAMALAKI--- --- ---MATEYUMARKOLUKAYOHANEMACHITIDWE A ATUMWIAROMA1 AKORINTO2 AKORINTOAGALATIYAAEFESOAFILIPIAKOLOSE1 ATESALONIKA2 ATESALONIKA1 TIMOTEO2 TIMOTEOTITOFILEMONIAHEBRIYAKOBO1 PETRO2 PETRO1 YOHANE2 YOHANE3 YOHANEYUDACHIVUMBULUTSO1 1 1 17 123456789101112131415161718192021222324252627282930311 1 1 : 1 123456789101112131415161718192021222324252627281 1 1 Buku Lopatulika MIYAMBO 17 Sungani Zolemba 1Nyenyeswa youma, pokhala mtendere, Iposa nyumba yodzala nyama yansembe, pali makangano.2Kapolo wocitamwanzeru Adzalamulira mwana wocititsa manyazi, Nadzagawana nao abale colowa.3Siliva ali ndi mbiya yosungunulira, golidi ali ndi ng'anjo; Koma Yehova ayesa mitima.4Wocimwa amasamalira milomo yolakwa; Wonama amvera lilime losakaza.5Wocitira ciphwete aumphawi atonza Mlengi; Wokondwera ndi tsoka sadzapulumuka cilango.6Zidzukulu ndizo korona wa okalamba; Ndipo ulemerero wa ana ndiwo atate ao.7Mlomo wangwiro suyenera citsiru; Ngakhale mlomo wonama suyenera kalonga ndi pang'ono ponse.8Wolandira cokometsera mlandu aciyesa ngale; Pali ponse popita iye acenjera.9Wobisa colakwa afunitsa cikondano; Koma wobwereza-bwereza mau afetsa ubwenzi.10Cidzudzulo cilowa m'kati mwa wozindikira, Kopambana ndi kukwapula wopusa kwambiri.11Woipa amafuna kupanduka kokha; Koma adzamtumizira mthenga wankhanza.12Kukomana ndi citsiru m'kupusa kwace Kuopsya koposa cirombo cocicotsera anace.13Wobwezera zabwino zoipa, Zoipa sizidzamcokera kwao.14Ciyambi ca ndeu cifanana ndi kutsegulira madzi; Tsono kupikisana kusanayambe tasiya makani.15Wokometsa mlandu wa wamphulupulu, ndi wotsutsa wolungama, Onse awiriwa amnyansa Yehova.16Kodi bwanji mtengo wogulira nzeru uli m'dzanja la citsiru, Popeza wopusa alibe mtima?17Bwenzi limakonda nthawi zonse; Ndipo mbale anabadwira kuti akuthandize pooneka tsoka.18Munthu wosowa nzeru apangana kulipirira wina, Napereka cikole pamaso pa mnzace.19Wokonda ndeu akonda kulakwa; Ndipo wotarikitsa khomo lace afunafuna kuonongeka.20Wokhota mtima sadzapeza bwino Ndipo mwini lilime lokhota adzagwa m'zoipa.21Wobala citsiru adzicititsa cisoni; Ndipo atate wa wopusa sakondwa.22Mtima wosekerera uciritsa bwino Koma mzimu wosweka uphwetsa mafupa,23Munthu woipa alandira cokometsera mlandu coturutsa m'mfunga, Kuti apambukitse mayendedwe a ciweruzo.24Nzeru iri pamaso pa wozindikira; Koma maso a wopusa ali m'malekezero a dziko.25Mwana wopusa acititsa atate wace cisoni, Namvetsa zowawa amace wombala.26Kulipiritsa wolungama sikuli kwabwino, Ngakhale kukwapula akuru cifukwa aongoka mtima.27Wopanda cikamwakamwa apambana kudziwa; Ndipo wofatsa mtima ali wanzeru.28Ngakhalecitsirucikatontholaaciyesa canzeru; Posunama ali wocenjera.Chewa Bible (BL) 1992 Zambia Bible Society, Malawi Bible Society and Zimbabwe Bible Society Buku Lopatulika MIYAMBO 17 00:00:00 00:00:00 0.5x 2.0x https://beblia.bible:81/BibleAudio/chewa1992/proverbs/017.mp3 31 17