× Chilankhulo Europe Chirasha Chibelarusi Chiyukireniya Chipolishi Chiserbia Chibugariya Chislovakia Czech Chiromani Chi Moldova Azerbaijan Chiameniya Chijojiya Chialubaniya Avar Bashkir Chitata Chechen Chisiloveniya Chiroatia ChiEstonia Chilativiya Chilithuania Chihangare Chifinishi Chinorway Chiswedwe Chi Icelandic Chi Greek Chimakedoniya Chijeremani Bavarian Chidatchi Chidanishi Chiwelsh Chi Gaelic Chiairishi Chifalansa Basque Chikatalani Chitaliyana Chitchainizi Achiroma Bosnian Kumpoto kwa Amerika Chingerezi South America Chisipanishi Chipwitikizi Chiguarani Quechuan Aymara Central America Chaku Jamaican Chilankhulo Chichewa Qeqchi Chaku Haiti Kum'mawa kwa Asia Chitchaina Chijapani Korea Chimongoliya Uyghur Hmong South East Asia Chimalaysian Chibama Chin Chinepali Cebuano Chitagalogi Wachikambodiya Chi Thai Chiindoneziya Chivietinamu Chijava Lao Iban IuMien Kachin Lahu Aceh Balinese Bugis Pampanga Sasak Shan Waray Kumwera kwa Asia Chihindi Оdia Awadhi Mizo Chikannada Malayalam Kambikatha Chimarathi Chigujarati Tamil Chilankhulo Chipunjabi Kurukh Assamese Maithili Chibengali Chiurdu Sinhala Dogri Haryanvi Meitei Konkani Santali Sindhi Koya Thado Sanskrit Devanagari Adilabad Gondi Ahirani Balochi Bundeli Chhattisgarhi Garhwali Kangri Kumaoni Mewari Munda Sadri Seraiki Shekhawati Sylheti Central Asia Chikigizi Chiuzbeki Chitajik Anthu aku Turkmen Kazakhstan Karakalpak Kuulaya Chituruki Chihebri Chiarabu Persian Chikurdi Chiashto Chikoputiki Africa Chiafrikaana Chixhosa Chizulu Ndebele Sotho Chiamhariki Wolaytta Waku Nigeria Mossi Ika Dinka Kabyle Ewe Chiswahili Morocco Wachisomali Chishona Madagascar Chiigbo Lingala Baoule Chiswati Chitsonga Chitswana Gambia Chiyoruba Kamba Chikinyarwanda Chihausa Chewa Chiluo Makua Dyula Fulfulde Kalenjin Kikuyu Kikwango Kirundi Krio Nigerian Pidgin Oromo Tshiluba Tshivenda Twi Umbundu Lugbara Luguru Pular Gussi Maasai Turkana Moba Nuer Shilluk Tamasheq Makonde Bemba Fon Hadiyya Ibibio Kimbundu Kimiiru Lango Liberian Kreyol Lomwe Mende Morisyen Ndau Nyankole Sena Sidamo Soga Songe Sukuma Tarifit Teso Tiv Zande Dagbani Dziko la Australia New Zealand Papua New Guinea Ziyankhulo Zakale Chiaramu Chilatini Chiesperanto 1 1 1 BL 1992 2016Buku Lopatulika 2014BL 1992BLYDC1 1 1 NYIMBO YA SOLOMONI GENESISEKSODOLEVITIKONUMERIDEUTERONOMOYOSWAOWERUZARUTE1 SAMUELE2 SAMUELE1 MAFUMU2 MAFUMU1 MBIRI2 MBIRIEZARANEHEMIYAESTEREYOBUMASALIMOMIYAMBOMLALIKINYIMBO YA SOLOMONIYESAYAYEREMIYAMALIROEZEKIELEDANIELEHOSEYAYOWELEAMOSIOBADIYAYONAMIKANAHUMUHABAKUKUZEFANIYAHAGAIZEKARIYAMALAKI--- --- ---MATEYUMARKOLUKAYOHANEMACHITIDWE A ATUMWIAROMA1 AKORINTO2 AKORINTOAGALATIYAAEFESOAFILIPIAKOLOSE1 ATESALONIKA2 ATESALONIKA1 TIMOTEO2 TIMOTEOTITOFILEMONIAHEBRIYAKOBO1 PETRO2 PETRO1 YOHANE2 YOHANE3 YOHANEYUDACHIVUMBULUTSO1 1 1 1 123456781 1 1 : 1 12345678910111213141516171 1 1 Buku Lopatulika NYIMBO YA SOLOMONI 1 Sungani Zolemba 1NYIMBO yoposa, ndiyo ya Solomo.2Mnyamatayo andipsompsonetse ndi m'kamwa mwace; Pakuti cikondi cako ciposa vinyo.3Mafuta ako anunkhira bwino; Dzina lako likunga mafuta onunkhira otsanulidwa; Cifukwa cace anamwali akukonda.4Undikoke; tikuthamangire; Mfumu yandilowetsa m'zipinda zace: Tidzasangalala ndi kukondwera ndi iwe. Tidzachula cikondi cako koposa vinyo: Akukonda molungama.5Wakuda ine, koma wokongola, Ana akazinu a ku Yerusalemu, Ngati mahema a Kedara, Ngati nsaru zociriga za Solomo.6Musayang'ane pa ine, pakuti ndada, Pakuti dzuwa landidetsa. Ana amuna a amai anandikwiyira, Anandisungitsa minda yamipesa; Koma munda wanga wanga wamipesa sindinausunga.7Ndiuze, iwe amene moyo wanga ukukonda, Umaweta kuti gulu lako? Umaligonetsa kuti pakati pa usana? Pakuti ndikhalirenji ngati wosocera Pambali pa magulu a anzako?8Ngati sudziwa, mkaziwe woposa kukongola, Dzituruka kukalondola bande la gululo, Nukawete ana a mbuzi zako pambali pa mahema a abusa.9Ndakulinganiza, wokondedwa wanga mnyamatawe, Ngati akavalo a magareta a Farao.10Masaya ako akongola ndi nkhata zatsitsi, Ndi khosi lako ndi zinganga za mkanda wonyezimira.11Tidzakupangira nkhata zagolidi Ndi njumu zasiliva.12Pokhala mfumu podyera pace, Mphoka yanga inanunkhira.13Wokondedwa wanga mnyamatayo ali kwa ine ngati thumba la nipa, Logona pakati pa maere anga.14Wokondedwa wanga ali kwa ine ngati cipukutu ca maluwa ofiira M'minda yamipesa ya ku Engedi.15Taona, wakongolatu, bwenzi langa; namwaliwe taona, wakongola, Maso ako akunga a nkhunda.16Taona, wakongolatu, bwenzi langa, mnyamatawe, inde, wakongoletsa; Pogona pathu mpa msipu.17Mitanda ya nyumba zathu nja mikungudza, Ndi mapaso athu nga mlombwa.Chewa Bible (BL) 1992 Zambia Bible Society, Malawi Bible Society and Zimbabwe Bible Society Buku Lopatulika NYIMBO YA SOLOMONI 1 00:00:00 00:00:00 0.5x 2.0x https://beblia.bible:81/BibleAudio/chewa1992/songofsolomon/001.mp3 8 1