× Chilankhulo Europe Chirasha Chibelarusi Chiyukireniya Chipolishi Chiserbia Chibugariya Chislovakia Czech Chiromani Chi Moldova Azerbaijan Chiameniya Chijojiya Chialubaniya Avar Bashkir Chitata Chechen Chisiloveniya Chiroatia ChiEstonia Chilativiya Chilithuania Chihangare Chifinishi Chinorway Chiswedwe Chi Icelandic Chi Greek Chimakedoniya Chijeremani Bavarian Chidatchi Chidanishi Chiwelsh Chi Gaelic Chiairishi Chifalansa Basque Chikatalani Chitaliyana Chitchainizi Achiroma Bosnian Kumpoto kwa Amerika Chingerezi South America Chisipanishi Chipwitikizi Chiguarani Quechuan Aymara Central America Chaku Jamaican Chilankhulo Chichewa Qeqchi Chaku Haiti Kum'mawa kwa Asia Chitchaina Chijapani Korea Chimongoliya Uyghur Hmong South East Asia Chimalaysian Chibama Chin Chinepali Cebuano Chitagalogi Wachikambodiya Chi Thai Chiindoneziya Chivietinamu Chijava Lao Iban IuMien Kachin Lahu Aceh Balinese Bugis Pampanga Sasak Shan Waray Kumwera kwa Asia Chihindi Оdia Awadhi Mizo Chikannada Malayalam Kambikatha Chimarathi Chigujarati Tamil Chilankhulo Chipunjabi Kurukh Assamese Maithili Chibengali Chiurdu Sinhala Dogri Haryanvi Meitei Konkani Santali Sindhi Koya Thado Sanskrit Devanagari Adilabad Gondi Ahirani Balochi Bundeli Chhattisgarhi Garhwali Kangri Kumaoni Mewari Munda Sadri Seraiki Shekhawati Sylheti Central Asia Chikigizi Chiuzbeki Chitajik Anthu aku Turkmen Kazakhstan Karakalpak Kuulaya Chituruki Chihebri Chiarabu Persian Chikurdi Chiashto Chikoputiki Africa Chiafrikaana Chixhosa Chizulu Ndebele Sotho Chiamhariki Wolaytta Waku Nigeria Mossi Ika Dinka Kabyle Ewe Chiswahili Morocco Wachisomali Chishona Madagascar Chiigbo Lingala Baoule Chiswati Chitsonga Chitswana Gambia Chiyoruba Kamba Chikinyarwanda Chihausa Chewa Chiluo Makua Dyula Fulfulde Kalenjin Kikuyu Kikwango Kirundi Krio Nigerian Pidgin Oromo Tshiluba Tshivenda Twi Umbundu Lugbara Luguru Pular Gussi Maasai Turkana Moba Nuer Shilluk Tamasheq Makonde Bemba Fon Hadiyya Ibibio Kimbundu Kimiiru Lango Liberian Kreyol Lomwe Mende Morisyen Ndau Nyankole Sena Sidamo Soga Songe Sukuma Tarifit Teso Tiv Zande Dziko la Australia New Zealand Papua New Guinea Ziyankhulo Zakale Chiaramu Chilatini Chiesperanto 1 1 1 BL 1992 2016Buku Lopatulika 2014BL 1992BLYDC1 1 1 MALIRO GENESISEKSODOLEVITIKONUMERIDEUTERONOMOYOSWAOWERUZARUTE1 SAMUELE2 SAMUELE1 MAFUMU2 MAFUMU1 MBIRI2 MBIRIEZARANEHEMIYAESTEREYOBUMASALIMOMIYAMBOMLALIKINYIMBO YA SOLOMONIYESAYAYEREMIYAMALIROEZEKIELEDANIELEHOSEYAYOWELEAMOSIOBADIYAYONAMIKANAHUMUHABAKUKUZEFANIYAHAGAIZEKARIYAMALAKI--- --- ---MATEYUMARKOLUKAYOHANEMACHITIDWE A ATUMWIAROMA1 AKORINTO2 AKORINTOAGALATIYAAEFESOAFILIPIAKOLOSE1 ATESALONIKA2 ATESALONIKA1 TIMOTEO2 TIMOTEOTITOFILEMONIAHEBRIYAKOBO1 PETRO2 PETRO1 YOHANE2 YOHANE3 YOHANEYUDACHIVUMBULUTSO1 1 1 1 123451 1 1 : 1 123456789101112131415161718192021221 1 1 Buku Lopatulika MALIRO 1 Sungani Zolemba 1Ha! mudziwo unadzala anthu, ukhalatu pa wokha! Ukunga mkazi wamasiye! Waukuruwo mwa amitundu, kalonga wamkazi m'madera a dziko Wasanduka wolamba!2Uliralira usiku; misozi yace iri pa masaya ace; Mwa onse amene anaukonda mulibe mmodzi wakuutonthoza: Mabwenzi ace onse aucitira ziwembu, Asanduka adani ace.3Yuda watengedwa ndende cifukwa ca msauko ndi ukapolo waukuru; Akhala mwa amitundu, sapeza popuma; Onse akumlondola anampeza pakati popsinjikiza.4M'njira za Ziyoni mulira posoweka akudzera msonkhano; Pa zipata zace zonse papasuka; ansembe ace onse ausa moyo; Anamwali ace asautsidwa; iye mwini namva zowawa.5Amaliwongo ace asanduka akuru ace, adani ace napindula; Pakuti Yehova wamsautsa pocuruka zolakwa zace; Ana ace ang'ono alowa m'ndende pamaso pa adani ace.6Ulemu wace wonse wamcokera mwana wamkazi wa Ziyoni; Akalonga ace asanduka nswala zosapeza busa, Anayenda opanda mphamvu pamaso pa wompitikitsa.7M'masiku a msauko wace ndi kusocera kwace Yerusalemu ukumbukira zokondweretsa zace zonse zacikhalire; Pogwidwa anthu ace ndi mdaniyo popanda wakuupulumutsa, Adaniwo anamuona naseka mwacipongwe mabwinja ace.8Yerusalemu wacimwa kwambiri; cifukwa cace wasanduka cinthu conyansa; Onse akuulemekeza aupeputsa, pakuti auona wamarisece; Inde, uusa moyo, nubwerera m'mbuyo.9Udio wace unali m'nsaru zace; sunakumbukira citsiriziro cace; Cifukwa cace watsika mozizwitsa; ulibe wakuutonthoza; Taonani Yehova, msauko wanga, pakuti mdaniyo wadzikuzayekha.10Amaliwongo atambasulira manja ao pa zokondweretsa zace zonse; Pakuti waona amitundu atalowa m'malo ace opatulika, Amene munalamulira kuti asalowe mumsonkhano mwanu.11Anthu ace onse ausa moyo nafunafuna mkate; Ndi zokondweretsa zao agula zakudya kuti atsitsimutse moyo wao; Taonani, Yehova, nimupenye; pakuti ndasanduka wonyansa.12Kodi muyesa cimeneci cabe, nonsenu opita panjira? Penyani nimuone, kodi ciripo cisoni cina ngati cangaci amandimvetsa ine, Cimene Yehova wandisautsa naco tsiku la mkwiyo wace waukali?13Anatumiza moto wocokera kumwamba kulowa m'mafupa anga, unawagonjetsa; Wachera mapazi anga ukonde, wandibwezera m'mbuyo; Wandipululutsa ndi kundilefula tsiku lonse.14Gori la zolakwa zanga lamangidwa ndi dzanja lace; Zalukidwa, zakwera pakhosi panga; iye wakhumudwitsa mphamvuyanga; Ambuye wandipereka m'manja mwao, sindithai kuwalaka.15Ambuye wapepula ngwazi zanga zonse pakati panga; Waitanira msonkhano pa ine kuti uphwanye anyamata anga, Ambuye wapondereza namwaliyo, mwana wamkazi wa Ziyoni, monga mopondera mphesa.16Cifukwa ca zimenezi ndilira; diso langa, diso langatu likudza madzi: Pakuti wonditonthoza, wotsitsimutsa moyo wanga, anditarikira; Ana anga asungulumwa, pakuti adaniwo apambana.17Ziyoni atambasula manja ace, palibe wakumtonthoza; Yehova walamulira kuti omzungulira Yakobo akhale adani ace; Yerusalemu wasanduka cinthu conyansa pakati pao.18Yehova ali wolungama; pakuti ndapikisana ndi m'kamwa mwace: Mudtvetu, mitundu ya anthu nonsenu, nimuone cisoni canga; Anamwali ndi anyamata anga atha kulowa m'ndende.19Ndinaitanaakundikondawokoma anandinyenga; Ansembe ndi akulu anga anamwalira m'mudzimu, Alikufunafuna zakudya zotsitsimutsa miyoyo yao.20Onani, Yehova; pakuti ndabvutika, m'kati mwanga mugwedezeka; Mtima wanga wasanduka mwa ine; pakuti ndapikisana nanu ndithu; Kunjako lupanga limangopha ana; m'nyumba muli imfa.21Iwo anamva kuti ndiusa moyo, palibe wonditonthoza; Adani anga onse atha kumva msauko wanga, nakondwera kuti mwatero ndinu; Mudzafikitsa tsiku lija mwalichula, ndipo iwowo adzanga ine.22Zoipa zao zonse zidze pamaso panu, Muwacitire monga mwandicitira ine cifukwa ca zolakwa zanga zonse, Pakuti ndiusa moyo kwambiri, ndi kulefuka mtima wanga,Chewa Bible (BL) 1992 Zambia Bible Society, Malawi Bible Society and Zimbabwe Bible Society Buku Lopatulika MALIRO 1 00:00:00 00:00:00 0.5x 2.0x https://beblia.bible:81/BibleAudio/chewa1992/lamentations/001.mp3 5 1