× Chilankhulo Europe Chirasha Chibelarusi Chiyukireniya Chipolishi Chiserbia Chibugariya Chislovakia Czech Chiromani Chi Moldova Azerbaijan Chiameniya Chijojiya Chialubaniya Avar Bashkir Chitata Chechen Chisiloveniya Chiroatia ChiEstonia Chilativiya Chilithuania Chihangare Chifinishi Chinorway Chiswedwe Chi Icelandic Chi Greek Chimakedoniya Chijeremani Bavarian Chidatchi Chidanishi Chiwelsh Chi Gaelic Chiairishi Chifalansa Basque Chikatalani Chitaliyana Chitchainizi Achiroma Bosnian Kumpoto kwa Amerika Chingerezi South America Chisipanishi Chipwitikizi Chiguarani Quechuan Aymara Central America Chaku Jamaican Chilankhulo Chichewa Qeqchi Chaku Haiti Kum'mawa kwa Asia Chitchaina Chijapani Korea Chimongoliya Uyghur Hmong South East Asia Chimalaysian Chibama Chin Chinepali Cebuano Chitagalogi Wachikambodiya Chi Thai Chiindoneziya Chivietinamu Chijava Lao Iban IuMien Kachin Lahu Aceh Balinese Bugis Pampanga Sasak Shan Waray Kumwera kwa Asia Chihindi Оdia Awadhi Mizo Chikannada Malayalam Kambikatha Chimarathi Chigujarati Tamil Chilankhulo Chipunjabi Kurukh Assamese Maithili Chibengali Chiurdu Sinhala Dogri Haryanvi Meitei Konkani Santali Sindhi Koya Thado Sanskrit Devanagari Adilabad Gondi Ahirani Balochi Bundeli Chhattisgarhi Garhwali Kangri Kumaoni Mewari Munda Sadri Seraiki Shekhawati Sylheti Central Asia Chikigizi Chiuzbeki Chitajik Anthu aku Turkmen Kazakhstan Karakalpak Kuulaya Chituruki Chihebri Chiarabu Persian Chikurdi Chiashto Chikoputiki Africa Chiafrikaana Chixhosa Chizulu Ndebele Sotho Chiamhariki Wolaytta Waku Nigeria Mossi Ika Dinka Kabyle Ewe Chiswahili Morocco Wachisomali Chishona Madagascar Chiigbo Lingala Baoule Chiswati Chitsonga Chitswana Gambia Chiyoruba Kamba Chikinyarwanda Chihausa Chewa Chiluo Makua Dyula Fulfulde Kalenjin Kikuyu Kikwango Kirundi Krio Nigerian Pidgin Oromo Tshiluba Tshivenda Twi Umbundu Lugbara Luguru Pular Gussi Maasai Turkana Moba Nuer Shilluk Tamasheq Makonde Bemba Fon Hadiyya Ibibio Kimbundu Kimiiru Lango Liberian Kreyol Lomwe Mende Morisyen Ndau Nyankole Sena Sidamo Soga Songe Sukuma Tarifit Teso Tiv Zande Dziko la Australia New Zealand Papua New Guinea Ziyankhulo Zakale Chiaramu Chilatini Chiesperanto 1 1 1 Buku Lopatulika 2014 2016Buku Lopatulika 2014BL 1992BLYDC1 1 1 YOBU GENESISEKSODOLEVITIKONUMERIDEUTERONOMOYOSWAOWERUZARUTE1 SAMUELE2 SAMUELE1 MAFUMU2 MAFUMU1 MBIRI2 MBIRIEZARANEHEMIYAESTEREYOBUMASALIMOMIYAMBOMLALIKINYIMBO YA SOLOMONIYESAYAYEREMIYAMALIROEZEKIELEDANIELEHOSEYAYOWELEAMOSIOBADIYAYONAMIKANAHUMUHABAKUKUZEFANIYAHAGAIZEKARIYAMALAKI--- --- ---MATEYUMARKOLUKAYOHANEMACHITIDWE A ATUMWIAROMA1 AKORINTO2 AKORINTOAGALATIYAAEFESOAFILIPIAKOLOSE1 ATESALONIKA2 ATESALONIKA1 TIMOTEO2 TIMOTEOTITOFILEMONIAHEBRIYAKOBO1 PETRO2 PETRO1 YOHANE2 YOHANE3 YOHANEYUDACHIVUMBULUTSO1 1 1 8 1234567891011121314151617181920212223242526272829303132333435363738394041421 1 1 : 1 123456789101112131415161718192021221 1 1 Buku Lopatulika YOBU 8 Sungani Zolemba 1Pamenepo anayankha Bilidadi Msuki, nati,2Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati namondwe kufikira liti?3Ngati Mulungu akhotetsa chiweruzo? Ngati Wamphamvuyonse akhotetsa mlandu?4Chinkana ana ako anamchimwira Iye, ndipo anawapereka mwa kulakwa kwao;5koma ukafunitsitsa Mulungu, ndi kupembedza Wamphamvuyonse;6ukakhala woyera ndi woongoka mtima, zoonadi adzakugalamukira tsopano, ndi kupindulitsa pokhala pako polungama.7Ndipo chinkana chiyambi chako chinali chaching'ono, chitsiriziro chako chidzachuluka kwambiri.8Pakuti ufunsire tsono mbadwo wapitawo, nusamalire zimene makolo ao adazisanthula.9Pakuti ife ndife adzulo, osadziwa kanthu, popeza masiku athu a pa dziko lapansi ndiwo ngati mthunzi;10amene aja sangakuphunzitse, ndi kukufotokozera, ndi kutulutsa mau a mumtima mwao?11Ngati gumbwa aphuka popanda chinyontho? Ngati manchedza amera popanda madzi?12Akali auwisi, sanawacheke, auma, asanaume mathengo onse ena.13Momwemo mayendedwe a onse oiwala Mulungu; ndi chiyembekezo cha onyoza Mulungu; chidzatayika.14Kulimbika mtima kwake kudzathyoka, chikhulupiriro chake chikunga nyumba ya kangaude.15Adzatsamira nyumba yake, koma yosamlimbira; adzaiumirira koma yosakhalitsa.16Akhala wamuwisi pali dzuwa, ndi nthambi zake zitulukira pamunda pake.17Mizu yake iyangayanga pa kasupe wamadzi, apenyerera pokhalapo miyala.18Akamuononga kumchotsa pamalo pake, padzamkana, ndi kuti, Sindinakuona.19Taona, ichi ndicho chomkondweretsa panjira pake, ndi panthaka padzamera ena.20Taona, Mulungu sakana munthu wangwiro; kapena kugwiriziza ochita zoipa.21Koma adzadzaza m'kamwa mwako ndi kuseka, ndi milomo yako kufuula.22Iwo akudana nawe adzavala manyazi; ndi hema wa oipa adzakhala kuli zii.Chewa Bible 2014 Bible Society of Malawi Buku Lopatulika YOBU 8 00:00:00 00:00:00 0.5x 2.0x https://beblia.bible:81/BibleAudio/chewa2014/job/008.mp3 42 8