Ndime ya TsikuOkutobala 8 EKSODO 15:13 Mwa chifundo chanu mwatsogolera anthu amene mudawaombola; mwamphamvu yanu mudawalondolera njira yakunka pokhala panu poyera. Chewa Bible 2014 Bible Society of Malawi