Ndime ya TsikuOgasiti 8 YOHANE 6:27 Gwirani ntchito si chifukwa cha chakudya chimene chitsalira kumoyo wosatha, chimene Mwana wa Munthu adzakupatsani inu; pakuti ameneyo Atate, ndiye Mulungu, adamlembera chizindikiro. Chewa Bible 2014 Bible Society of Malawi