Ndime ya TsikuSeputembala 9 AHEBRI 11:6 koma wopanda chikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa; pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti alipo, ndi kuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna Iye. Chewa Bible 2014 Bible Society of Malawi